Njira yoyambila: sambani mmanja na soap ndi madzi yotuba Njira Yachiwiri: Bwezaniponi njira yoyamba ๐Ÿ˜œ

Njira yoyambila: sambani mmanja na soap ndi madzi yotuba Njira Yachiwiri: Bwezaniponi njira yoyamba ๐Ÿ˜œ
Download Image

Manja yanu ni malo oyamba ponkhala kalombo ka COVID-19. Tiyeni tisamale manja athu kupyolera kusuka na soap ndi madzi pa nthawi mphindi makhumi yawiri.

โ€

Choonadi

Njira zisanu mosukila mmanja (โœ‹).
โ€

Sambani mmanja pa thanwi ya mpindi makhumi awiri, ngati sitelo, gwilisani nchito hand sanitizer ili na 60% moba. Valani mphuno ndi kamwa po khosola ndi kamboyo, osati manja. Osagwila menso, kamwa kapena mphuno. Talukani pakati kaanthu,makamaka baja ali na nthenda ya chifuwa. Nkhalani pa nyumba.

โ€

Kalombo ka COVID-19 kankala pa zintu zosiya mu nthawi ya maola 72. ย Njira izi zisanu zizateteza inu ku kalombo ka COVID-19.

โ€

https://www.cdc.gov/coronavirus/2019-ncov/prevent-getting-sick/prevention.html